Mbuzi, Galu ndi Ng’ombe anali mabwenzi kwambiri. Tsiku lina, anapita paulendo ndi galimoto.
Goat, Dog, and Cow
were great friends. One
day they went on a
journey in a taxi.
Imbushi, Imbwa ne ŋombe baali fibusa saana. Ubushiku bumo baile pa bulendo muli motoka.
Pamene anafika pothera pa ulendo wao, mtekenya anawafunsa kuti alipire ndalama. Ng’ombe inalipira yake.
When they reached the
end of their journey, the
driver asked them to
pay their fares. Cow
paid her fare.
Ilyo baafikile uko baaleya, namutekenya aabebele ukulipila indalama. Iŋombe yalilipiile.
Galu analipira ndalama yopitirirapo chifukwa analibe ndalama yoyenera.
Dog paid a bit extra,
because he did not
have the correct money.
Imbwa yaalipile indalama iikalamba pantu tayakwete indalama iinoono.
Mtekenya anali pafupi kupatsa Galu cenji yake pamene mbuzi inathawa kopanda kulipira.
The driver was about to
give Dog his change
when Goat ran away
without paying
anything.
Namutekenya cilya aalimukupeela Imbwa cenji, Imbushi yabutuka ukwabula ukulipila nangu lumo.
Mtekenya anakalipa kwambiri. Anayenda popanda kupatsa Galu chenji yake.
The driver was very
annoyed. He drove
away without giving
Dog his change.
Namutekenya tepakufulwa. Efyo aenseshe motoka ukwabula ukubwesesha Imbwa cenji.
Ndiye cifukwa cake, ngakhale lero lomwe, Galu amathamangira galimoto kuona mkati ndi kupeza mtekenya amene ali ndi cenji yake.
That is why, even
today, Dog runs
towards a car to peep
inside and find the
driver who owes him his
change.
Eco, mpaka na leelo, Imbwa ipepekela motoka pakuti imone mukati nga cakuti namutekenya uwaikwatila indalama emwali.
Mbuzi imathawa ikamvera galimoto. Imaopa kuti angaimangidwe chifukwa siinalipire mtekenya.
Goat runs away from
the sound of a car. She
is afraid she will be
arrested for not paying
her fare.
Imbushi ilabutuka iciunda ca motoka. Ilatiina ukuikata pa mulandu wa kukaana lipila indalama.
Ndipo Ng’ombe siimaikako nzelu ngati galimoto iri kubwela. Ng’ombe imayenda pang’ono pang’ono cifukwa idziwa kuti inalipira ndalama mokwana.
And Cow is not
bothered when a car is
coming. Cow takes her
time crossing the road
because she knows she
paid her fare in full.
Elyo Iŋombe yena taisakamana nangu motoka ileisa. Yendafye cilumba-cilumba pa kuciluka umusebo nangu motoka ileisa pantu yalishiba ukuti yalilipila indalama shonse.