Back to stories list

Mwana wa Bulu Donkey Child Umwana Punda

Written by Lindiwe Matshikiza

Illustrated by Meghan Judge

Translated by David Sani Mwanza

Read by Christine Mwanza

Language Nyanja

Level Level 3

Narrate full story The audio for this story is currently not available.


Kanali kamwana kakakazi kang’ono komwe kanaona cinthu ca maonekedwe odabwitsa patali.

It was a little girl who first saw the mysterious shape in the distance.

Umukashana umunoono ewabalilepo ukumona icintu cileisa akatalamukila.


Pamane cinthu cinabwela pafupi, anaona kuti anali mzimai omwe anali ndi mimba yaikulu.

As the shape moved closer, she saw that it was a heavily pregnant woman.

Ilyo ico cintu cafikile mupepi, aamwene ukuti ni namaayo uwali pabukulu.


Mwamanyazi koma mopanda mantha, kamwana kanasendera pafupi ndi mzimai. “Tifunika kuwasunga.,” anthu a kamwana kakazi anaganizira. “Tizamusunga ndi mwana wake bwino-bwino.

Shy but brave, the little girl moved nearer to the woman. “We must keep her with us,” the little girl’s people decided. “We’ll keep her and her child safe.”

Nangu umukashana aali ne nsoni alishipile no kupalama mupepi na namaayo. “Tufwile twamusunga uyu namaayo,” efyalandile abantu. “Tulemusunga bwino no mwana wakwe.”


Mwana anali pafupi kubadwa. “Kankha!” “Bwelesani zovimba!” “Manzi!” “Kankhaaaa!!!”

The child was soon on its way. “Push!” “Bring blankets!” “Water!” “Puuuuussssshhh!!!”

Papatafye akashita kanoono umwana aba munshila. “Sunka!” “Leeta amalangeti!” “Ameenshi!” “Suunkaa!!!”


Koma pamene anaona mwana wakhanda, aliyense analumpha modabwa. “Bulu?!”

But when they saw the baby, everyone jumped back in shock. “A donkey?!”

Nomba ilyo baamwene umwana, bonse batolokela kunuma mu kusunguka. “Punda?”


Aliyense anayamba kukangana. “Tinanena kuti tizasunga make pamozi ndi mwana wake bwino-bwino, ndipo tizacita motero,” ena anatero. “Koma azatibweretsera soka!” enanso ananena.

Everyone began to argue. “We said we would keep mother and child safe, and that’s what we’ll do,” said some. “But they will bring us bad luck!” said others.

Bonse baatampile ukupaashanya. “Twacitila tulesunga umwana na nyina bwino, kanshi efyo twalacita,” efyo abantu bamo basosa. “Nomba bakatuletela ishamo!” efyo bambi baasosele.


Cifukwa ca ico, mzimai anakhalanso yekha. Anabvutika kuganiza zomwe azacita ndi mwana wodabwisa. Anabvutika kuziganizira cocita..

And so the woman found herself alone again. She wondered what to do with this awkward child. She wondered what to do with herself.

Efyo nomba namaayo aisangile eka na kabili. Taishibe ifyakucita no mwana wa musango uyu. Taishibe ifyakucita umwine.


Koma pothera, anavomera kuti bulu anali mwana wake ndipo anali mai wake.

But finally she had to accept that he was her child and she was his mother.

Panuma aasuminafye ukuti umwana aali mwana wakwe elyo nao ali ni nyina.


Tsopano, ngati mwana anakhala cimodzimodzi, ndi thupi ing’ono, zinthu zinakakhalako mosiyana. Koma bulu anakula ndi kukula kufikira nthawi yomwe sankakhala pa msana pa mai wake. Ndipo mkhalidwe wake unasiyana ndi munthu. Amai ake anli olema nthawi zambriri komanso aukali. Nthawi zina, anatuma mwana kucita nchito zomwe zinafunikira kucitika ndi nyama.

Now, if the child had stayed that same, small size, everything might have been different. But the donkey child grew and grew until he could no longer fit on his mother’s back. And no matter how hard he tried, he could not behave like a human being. His mother was often tired and frustrated. Sometimes she made him do work meant for animals.

Nomba nga cakuti umwana taaleekula, alifye umunono, fyonse nga fyalifye bwino. Lelo uyu punda alikulile saana icakuti aleka ukukumana mu numa yaba nyina. Elyo nangu eshe shani, ificitwa fyakwe tafyali fya buntu. Inshita yonse banyina baleebafye ne cifukushi kabili abanaka. Limo-limo baaleemupeela incito sha nama.


Msokonezo ndi mkwiyo unakula mu mtima wa bulu. Anali kulephela kucita zirizonse. Analephela kukhali ndi mkhalidwe weni weni. Anali okwiya kotero kuti, tsiku lina, anamenyela amai ake pansi.

Confusion and anger built up inside Donkey. He couldn’t do this and he couldn’t do that. He couldn’t be like this and he couldn’t be like that. He became so angry that, one day, he kicked his mother to the ground.

Punda alifye awakalipa, taishibe ifyakucita kabili aatampile ukumfwa icifukushi. Teti acite icili conse. Teti abe ifili fyonse. Alifulilwe saana icakuti, ubushiku bumo, alipantile banyina bapona na panshi.


Bulu anacita manyazi. Anayamba kuthawira kutali komwe angathe kupita.

Donkey was filled with shame. He started to run away as far and fast as he could.

Punda alyumfwile insoni. Aatampile ukubutuka ukuya ukutali saana.


Pa nthawi imene analeka kuthamanga, unali usiku, Bulu anasowa. “Hee, hyu?” ananong’oneza ku mdima. Anafika pamathero. Anayamba kusanduka. Anagona mu tulo twatukulu twa mabvuto.

By the time he stopped running, it was night, and Donkey was lost. “Hee haw?” he whispered to the darkness. “Hee Haw?” it echoed back. He was alone. Curling himself into a tight ball, he fell into a deep and troubled sleep.

Ilyo Punda alekele ukubutuka, ninshi nakufiita, taishiibe uko aali. “Hee haw?” efyo aitootoosha mumfifi. “Hee Haw?” aumfwa iciunda. Ali eka. Aipeta, apona na mutulo utwinetwine utwamalangulushi.


Bulu anauka ndi kupeza nkhalamba iri kumuyangana. Anayangana mu maso a nkhalambayo ndi kuyamba kukhala ndi ciyembekezo.

Donkey woke up to find a strange old man staring down at him. He looked into the old man’s eyes and started to feel a twinkle of hope.

Punda ukubuuka asanga shikulu-bantu uo ashaishibe aleemulolesha. Alolesha mu menso yakwa shikulu-bantu amona ukuti kuti amwafwilisha.


Bulu anapita kukakhala ndi nkhalamba ija, imene inam’phunzitsa njira zambiri zomwe angakhaliremo. Bulu anamvetsera ndi kuphunzira, cimodzi-modzi nkhalamba nayenso inamvetsera ndi kuphunzira. Anathandizana ndipo anaseka pamodzi.

Donkey went to stay with the old man, who taught him many different ways to survive. Donkey listened and learned, and so did the old man. They helped each other, and they laughed together.

Punda aile mu kwikala na shikulu-bantu, uwamufundile inshila sha kwikalilamo ishingi. Punda aaleumfwa no kusambilila, shikulu-bantu nao wine aaleesambilila. Baleyafwana no kusekela pamo.


Tsiku lina m’mawa, nkhaalamba inapempha Bulu kuti ainyamule kuipereka pa mwamba pa phiri.

One morning, the old man asked Donkey to carry him to the top of a mountain.

Ubushiku bumo, shikulu-bantu aipwishe punda ukumusenda pa muulu wa lupili.


Pamwamba pa mithambo, anagona. Bulu analota kuti amai ake anali kudwala ndipo anali kumuitana. Ndipo pamene anauka…

High up amongst the clouds they fell asleep. Donkey dreamed that his mother was sick and calling to him. And when he woke up…

Pa muulu mu makumbi basendama. Punda aalotele ukuti banyina nabalwala kabili balemwita. Ilyo abukile…


….Mithambo inasowa pamozi ndi mzake, nkaalamba ija.

… the clouds had disappeared along with his friend, the old man.

… asangile amakumbi nayaluba pamo no munankwe, shikulu- bantu.


Bulu pomaliza anadziwa zomwe anafunika kucita.

Donkey finally knew what to do.

Panuma Punda alishibe ifyakucita.


Bulu anapeza amai ake, okha ali kulirira mwana wao wosowa. Anapenyana kwakanthawi. Kenaka anakumbatirana mwamphamvu.

Donkey found his mother, alone and mourning her lost child. They stared at each other for a long time. And then hugged each other very hard.

Punda aasangile banyina, beka baleeloosha umwana uwalubile. Baliloleshanya akashita akatali. Elyo bakumbatana saana.


Bulu ndi amai ake akulira pamozi ndipo anapeza njira zosiyana-siyana zokhaliramo pamodzi. Pang’ono pang’ono, onse anthu okhala pafupi nao, mabanja lao anayamba kukhala nao pamozi mopanda vuto leni-leni.

The donkey child and his mother have grown together and found many ways of living side by side. Slowly, all around them, other families have started to settle.

Umwana Punda na banyina balikulila pamo elyo kabili balisanga inshila ishingi ishakwikalilamo bwino pamo. Panoono-panoono, bonse ababashinguluka, na balupwa balitampa ukwikala bwino.


Written by: Lindiwe Matshikiza
Illustrated by: Meghan Judge
Translated by: David Sani Mwanza
Read by: Christine Mwanza
Language: Nyanja
Level: Level 3
Source: Donkey Child from African Storybook
Creative Commons License
This work is licensed under a Creative Commons Attribution 4.0 International License.
Options
Back to stories list Download PDF